Timakonza ma TV, ma charger, ma speaker, ndi zipangizo zina kuti zibwerere kugwira ntchito bwino.
Kuyika ma socket, ma switch, ma light, ndi wiring yotetezeka ya kunyumba kapena shopu.
Zida zatsopano ndi accessories: ma adapter, ma earphones, ma power bank, ma inverter ndi zina.